N’ciani Catsopano?
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Zimene Mungacite pa Kuwelenga Kwanu—Onetsani Kulimba Mtima Mukapanikizika
Kodi tingaphunzileponji pa kulimba mtima komwe anaonetsa Yeremiya ndi Ebedi-meleki?
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Funso Losavuta Limene Lingakhale ndi Zotulukapo Zabwino
Monga zinalili ndi Mary, inunso mukhoza kuyambitsa maphunzilo a Baibulo mwa kufunsa funso losavuta.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Mmene Mungakhalile Bwenzi Lenileni
Baibulo limaonetsa kuti kukhala ndi mabwenzi enieni m‘nthawi ya mavuto n’kofunika kwambili.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Pewani Mzimu Wodzikonda Umene Wafala Masiku Ano
Anthu ambili masiku ano amaganiza kuti ayenela kupatsidwa maudindo apadela, komanso kucitilidwa zinthu m’njila yapadela kuposa ena. Onankoni zina mwa mfundo za m’Baibulo zimene zingatithandize kupewa kaganizidwe ka conco.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
“Sindinakhalepo Ndekhandekha”
Onani cifukwa cake Angelito Balboa amakhulupilila kuti Yehova anali naye nthawi zonse, ngakhale pamene anakumana mayeso ovuta.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
February 2025
Magazini ino ili ndi nkhani zophunzila mu mlungu wa April 14–May 4, 2025.
UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO
March–April 2025
NKHANI ZATSOPANO
Ciunikilo Na 7 ca Bungwe Lolamulila mu 2024.
Mu Ciunikilo cino, tiimve mmene zinthu zilili kwa abale ndi alongo athu m’maiko osiyanasiyana. Kuonjezela apo, tikhalenso ndi mwayi wokambilana ndi abale awili, m’bale Jody Jedele ndi m’bale Jacob Rumph amene ndi mamembala atsopano a Bungwe lolamulila.
KHALANI MASO!
Nyama Zakuchile Zacepa ndi 73 Pelesenti m’Zaka 50—Kodi Baibulo Likutipo Ciyani?
Baibulo limapeleka ciyembekezo cabwino cokhudza nyama zakuchile.
MAFUNSO AMENE AMAFUNSIDWA KAŴILI-KAŴILI
Kodi a Mboni za Yehova Amaphunzitsidwa Bwanji Mmene Angacitile Utumiki Wawo?
Kodi timaphunzila bwanji kulalikila ndi kuphunzitsa?