Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.
Uganda
808 Lubowa Estate Road
Lubowa
KAMPALA
UGANDA
+256 41-4-201-194
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.
Nthawi yoona malo: Mphindi 30
Zimene Timacita
Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’zinenelo 8 za m’dzikoli. Zinenelo zimenezo ndi Ciacoli, Ciateso, Cihukonzo, Ciluganda, Cilugibara, Cimadi, Cirunyankore, ndi Cirutoro.