Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

The Democratic Republic of the Congo

75, 13e Rue, Q. Industriel

LIMETE

KINSHASA

DEMOCRATIC REPUBLIC OF THE CONGO

+243 81-555-1000

+243 99-818-9791

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:30hrs mpaka 10:30hrs ndi 13:30hrs mpaka 15:30hrs.

Nthawi yoona malo: Ola limodzi

Zimene Timacita

Timamasulila magazini a Nsanja ya Mlonda m’zinenelo 7 ndi mabuku ena m’zinenelo zina 27. Timatumiza matani 1,670 a mabuku kumipingo yoposa 3,000 caka ciliconse m’dziko lathu.

Tengani kapepala koonetsa malo.