Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.
Burundi
Les Témoins de Jéhovah
Uprona Boulevard
Corner of Muyinga Ave., Rohero II
BUJUMBURA
BURUNDI
+257 2224-1110
+257 2224-5564
+257 2224-8112
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs
Nthawi yoona malo: Ola limodzi
Zimene Timacita
Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’Cikirundi ndi kupanga ma CD a zofalitsa za cinenelo cimeneci. Timatumiza zofalitsa m’mipingo ndi magulu oposa 280.