Uzidekha
Mawu a Nyimbo:
1. Poyenda uzidekha,
Inde n’zovuta kuziletsa.
Ngati uli na mabwenzi,
Kuno simalo ya maseŵela.
(KOLASI)
Uzidekha
Ucite zinthu bwino.
Ukonde nchito yako
Uzidekha.
2. Zocita ni zambili,
Mpingo wonse ukudalila.
Kumbukila abale,
Uŵakonde nakuceza nawo.
(KOLASI)
Uzidekha
Ucite zinthu bwino.
Ukonde nchito yako
Uzidekha
3. Ungafike panyumba
Kodi alipo olo palibe?
Udziona ali pafupi
Ukambenso na oyenda mu njila.
(KOLASI)
Uzidekha
Ucite zinthu bwino.
Ukonde nchito yako
Uzidekha.
Uzidekha.