Za m’Kope Ino ya Galamuka!: Kodi Baibo Ingakuthandizeni Kukhala na Umoyo Wabwino?
Buku Lakale-kale, Koma Lothandiza Masiku Ano
Baibo imatiuza mmene tingalambilile Mulungu. Ilinso na malangizo othandiza mu umoyo wathu wa tsiku na tsiku, monga m’mbali izi:
Thanzi labwino
Kudziŵa kulamulila mtima wathu
Umoyo wa banja komanso mabwenzi
Moseŵenzetsela ndalama
Umoyo wauzimu
Buku Lothandiza Kwambili m’Mbili Yonse ya Anthu
Kwa zaka zambili, Baibo yathandiza anthu kukhala na umoyo wabwino. Masiku ano, imapezeka m’vitundu vambili. Dziŵani mmene mungapindulile na malangizo a m’Baibo othandiza.