ZOTI MUCHITE Zimene Mungachite Kuti Muzigwiritsa Ntchito Bwino Ndalama YAMBANI Zoti muchitezi zikuthandizani kuti muzigwiritsa ntchito bwino ndalama zanu. Pangani Dawunilodi Nkhani Zina Zoti Achinyamata Achite Achinyamata Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndingatani Kuti Ndisamawononge Ndalama? Kodi nthawi ina munapitapo mu shopu kuti mukangoona zinthu koma n’kugula chinthu chodula kwambiri? Ngati ndi choncho, nkhaniyi ikuthandizani. MAVIDIYO AMAKATUNI Mungatani Kuti Muzigwiritsa Ntchito Bwino Ndalama Zanu? Muzisunga bwino ndalama zanu kuti zidzakuthanizeni mukadzafuna kuzigwiritsa ntchito. KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO Kodi Baibulo Lingathandize pa Nkhani ya Mavuto Azachuma Ndiponso Ngongole? Ndalama sizingakuthandizeni kukhala wosangalala koma pali mfundo za m’Baibulo zinayi zimene zingakuthandizeni pa mavuto azachuma. NKHANI ZINA Zimene Mungachite Ngati Mukupeza Ndalama Zochepa Mavuto azachuma akabwera mwadzidzidzi zimadetsa nkhawa, koma mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kuti muzitha kugwiritsa ntchito ndalama zochepa. NSANJA YA OLONDA Kodi Mungatani Kuti Muzigula Zinthu Mogwirizana Ndi Ndalama Zimene Mumapeza? Patsani ena Patsani ena Zimene Mungachite Kuti Muzigwiritsa Ntchito Bwino Ndalama ZOTI ACHINYAMATA ACHITE Zimene Mungachite Kuti Muzigwiritsa Ntchito Bwino Ndalama Chichewa Zimene Mungachite Kuti Muzigwiritsa Ntchito Bwino Ndalama https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502017204/univ/art/502017204_univ_sqr_xl.jpg