Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Nkhani Zomwe Zangoikidwa Kumene Patsamba Loyamba la Webusaiti Yathu

 

Makhalidwe Abwino Angakuthandizeni Kuti Muzisangalala

Anthu ambiri amayendera mfundo yoti: ‘Palibe vuto ndi kuchita chilichonse chomwe mtima wako ukufuna, bola ngati iweyo ukuona kuti n’choyenera.’ Koma kodi ndi nzeru kutsatira mfundo imeneyi? Werengani nkhaniyi kuti muone makhalidwe ena a m’Baibulo amene angakuthandizeni.

Mungatani Kuti Musayambe Kumwa Mowa Mopitirira Malire?

Mfundo 5 zimene zingakuthandizeni kuti musamamwe mowa mopitirira malire ngakhale pamene muli ndi nkhawa kwambiri.

Vuto Losungulumwa Padziko Lonse

Kodi mungathane nalo bwanji?

 

Kodi Ulemu Unapita Kuti?

Onani zimene zingakuthandizeni kuti muzidzilemekeza, muzilemekeza ena komanso kuti muzilemekeza moyo.

 

N’chifukwa Chiyani Timafunikira Mulungu?

Werengani kuti mudziwe mmene kukhala pa ubwenzi ndi Mulungu kungatithandizire kuti tikhale ndi moyo wosangalala.

Ndingatani Ngati Anthu Ena Amandivutitsa pa Intaneti?

Zimene muyenera kuchita komanso zimene mungachite kuti mudziteteze.

Kuti Mutsanzire Yesu Muyenera . . .

Nthawi zonse Yesu ankasonyeza makhalidwe 8.

Kodi Mwambo wa Halowini Unayamba Bwanji?

Kodi kudziwa kuti Halowini inayambira kuchikunja kuli ndi vuto lililonse?

Kodi Baibulo Lingakuthandizeni Bwanji?

Kuti mudziwe zambiri, yambani kuphunzira Baibulo kwaulere kumene kumachitika mokambirana.

 

Kodi Zidzatheka Bwanji Kuti Padziko Lonse Lapansi Padzakhale Mtendere?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Mulungu walonjeza zoti Ufumu wake udzabweretsa mtendere padziko lapansili.

Mungakhale ndi Moyo Wosangalala

Magaziniyi ya Galamukani! Ikufotokoza mmene malangizo anzeru a m’Baibulo angakuthandizireni.