Kupanga Baibulo Latsopano YAMBANI Kupanga Baibulo Latsopano Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene zinachitika pokonza Baibulo la Dziko Latsopano la chingelezi la 2013. Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi NTCHITO YOFALITSA MABUKU Baibulo Lolimba Kwambiri Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lomwe linatulutsidwa mu 2013, ndi lolimba komanso lokongola kwambiri. NTCHITO YOFALITSA MABUKU Ofesi ya Mboni za Yehova ku Japan Ikusindikiza Mabaibulo a Zikuto Zolimba Omwe Akutumizidwa M’madera Osiyanasiyana Padziko Lapansili A Mboni za Yehova aika makina okonzera mabuku kufakitale yawo ya ku Japan. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zambiri zokhudza makina amenewa. MOYO WA PA BETELI Chionetsero Chapadera cha Baibulo Kuyambira kale, Yehova Mulungu wakhala akuuza anthu dzina lake. Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene omasulira Baibulo achita pofuna kuti dzina la Mulungu lisaiwalike. NTCHITO YOFALITSA MABUKU Tapatsidwa Ntchito Yomasulira “Mawu Opatulika a Mulungu”—Aroma 3:2 Kwa zaka zambiri, a Mboni za Yehova akhala akugwiritsira ntchito Mabaibulo osiyanasiyana. Koma n’chifukwa chiyani anaganiza zomasulira Baibulo m’Chingelezi chimene anthu amalankhula masiku ano? MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI Kodi Ndalama Zoyendetsera Ntchito ya a Mboni za Yehova Zimachokera Kuti? Dziwani mmene ntchito yolalikira padziko lonse ikuyendera bwino popanda kupemphetsa ndalama kapena kupereka chakhumi. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kupanga Baibulo Latsopano NTCHITO YOFALITSA MABUKU Kupanga Baibulo Latsopano Chichewa Kupanga Baibulo Latsopano https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502015161/univ/art/502015161_univ_sqr_xl.jpg