Mboni za Yehova Padziko Lonse

Vanuatu

  • Port-Vila, Vanuatu​—Akukambirana ndi munthu mfundo za m’Baibulo m’mudzi wa Eratap

Mfundo Zachidule—Vanuatu

  • 334,000—Chiwerengero cha anthu
  • 694—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 13—Mipingo
  • Pa anthu 560 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse

Alongo ambiri amene anasamukira kumayiko ena poyamba ankadzikayikira. Kodi anatani kuti alimbe mtima? Kodi aphunzirapo chiyani atatumikira kudziko lina?