Mfundo Zachidule—Cambodia
- 16,855,000—Chiwerengero cha anthu
- 1,116—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 17—Mipingo
- Pa anthu 15,295 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
GALAMUKANI!
Dziko la Cambodia
N’chifukwa chiyani anthu oti angokumana koyamba amatchulana kuti achimwene, chemwali, azakhali, amalume kapena agogo?
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Zimene Ndinasankha Ndili Mwana
Mnyamata wina wa ku Columbus, Ohio, U.S.A. anaganiza zophunzira Chikambodiya. N’chifukwa chiyani anachita zimenezi? Kodi zimenezi zinakhudza bwanji zimene anadzachita m’tsogolo?