Mfundo Zachidule—Ghana
- 33,063,000—Chiwerengero cha anthu
- 153,657—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 2,484—Mipingo
- Pa anthu 220 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Anadzipereka ndi Mtima Wonse—Ku Ghana
Anthu amene anasamukira m’mayiko ena amakumana ndi mavuto ambiri koma amadalitsidwanso kwabasi.