Mfundo Zachidule—Colombia
- 51,673,000—Chiwerengero cha anthu
- 186,712—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 2,271—Mipingo
- Pa anthu 279 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NKHANI
A Mboni Anapatsidwa Mphoto ndi Bungwe Loona Ntchito Yomasulira M’chinenero cha Manja ku Colombia
A Mboni za Yehova ku Colombia analandira mphoto ziwiri powayamikira chifukwa cha ntchito yawo yomasulira m’Chinenero Chamanja cha ku Colombia.