Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2011
Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2011
NYAMA NDI ZOMERA
Nyama Zokongola Mogometsa (Mahatchi a ku Arabia), 4/11
Mbalame N’zaluso pa Usodzi, 9/11
Khungwa la Mtengo, 7/11
Uchi wa Nyerere, 5/11
ZACHUMA NDI NTCHITO
Muzigwiritsa Ntchito Ndalama Mwanzeru, 9/11
ZOTI BANJA LIKAMBIRANE
1/11, 2/11, 3/11, 4/11, 5/11, 6/11, 7/11, 8/11, 9/11, 10/11, 11/11, 12/11
UMOYO NDI MANKHWALA
Khansa ya M’mawere, 8/11
Ngati Mwana Ali ndi Khansa, 5/11
Ana Obadwa ndi Matenda Ozerezeka, 6/11
Matenda a Chingwangwa, 11/11
Mfundo Zisanu Zokuthandizani Kukhala ndi Thanzi Labwino, 3/11
Kusamalira Mwapadera Munthu Wodwala Matenda Oti Sachira, 7/11
Mutu Waching’alang’ala, 1/11
Matenda a Pulositeti, 2/11
Kugona Mokwanira, 1/11
Nzeru Zothandiza Munthu Kukhala ndi Thanzi Labwino, 8/11
MAUNANSI A ANTHU
Kodi Mungaiwale Bwanji Imfa ya Munthu amene Mumamukonda? 4/11
Kulera Ana Kuti Akule Bwino, 10/11
Kulera Ana Obadwa ndi Matenda Ozerezeka, 6/11
MBONI ZA YEHOVA
Buku la Phunzirani kwa Mphunzitsi Waluso, 12/11
“Sindinkafuna Kulisiya” (Buku la Zimene Achinyamata Amadzifunsa, Gawo 2), 4/11
“Ufumu wa Mulungu Ubwere” Msonkhano Wachigawo, 5/11
“Mulembereni Kalata Anton” (Russia), 9/11
MAYIKO NDI ANTHU
Madzi osefukira ku Japan 2011, 12/11
Buku Lachiweruzo (England), 9/11
Uchi wa Nyerere (Australia), 5/11
Maulendo a Ibn Battuta, 8/11
Munthu Wokonda Kufunsa Mafunso (Nicarao wa ku Nicaragua), 12/11
Anatchona Kofunafuna Golide (Australia), 2/11
John Foxe Anakhala ndi Moyo pa Nthawi Yovuta Kwambiri (England), 11/11
Nsanja Zokongola za M’mapiri a Svaneti (Georgia), 6/11
Chakumwa cha ku Mexico (tequila), 11/11
Nyumba za Mbalame za ku Istanbul (Turkey), 1/11
Mathithi a Murchison Ndi Okongola Kwambiri (Uganda), 9/11
Luso la Zopangapanga la Anthu a ku Russia, 9/11
Zida Zoimbira za M’nthawi ya Aisiraeli, 3/11
Anthu a Mtundu wa Chitata, 9/11
Zojambula Zosangalatsa za Tingatinga (Tanzania), 11/11
Njira Yomwe Akapolo Ankadutsa (Benin), 5/11
Abusa a Nkhosa a ku Wales, 7/11
MBIRI YA MOYO WA ANTHU
Ndinadziwa Yemwe Adzathetse Kupanda Chilungamo (U. Menne), 11/11
Ndinali Munthu Woopsa Kwambiri (J. Nebrera), 4/11
Ndimasangalala Kuti Ndine M’busa (A. Bekmanov), 3/11
Moyo Wopindulitsa Kwambiri (H. Neuhardt), 2/11
Chipani cha Nazi Chinalephera Kundisintha (H. Liska), 8/11
Ndinapeza Chinthu Chamtengo Wapatali (M. Ibatullin), 6/11
ZOSIYANASIYANA
Ngozi Zapamsewu, 7/11
Mwana Akamabadwa, 1/11
Zolinga Zimene Mungathe Kuzikwaniritsa, 2/11
Mawotchi Amakedzana (mawotchi), 1/11
Mulungu Adzathetsa Mavuto Athu Onse, 7/11
Milomo Yanu Ndi “Ziwiya Zamtengo Wapatali,” 5/11
Nyimbo, 8/11
Zamatsenga, 2/11
Nyengo Inalepheretsa Anthu Kupambana Nkhondo Zikuluzikulu, 6/11
CHIPEMBEDZO
Zifukwa Zomveka Zokhulupirira Kuti Kuli Mulungu 11/11
Buku Limene Lapulumuka Zambiri (Baibulo), 12/11
Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira (Baibulo), 1/11, 2/11, 3/11, 4/11, 5/11
Mtengo wa Khirisimasi, 12/11
Kodi Zipembedzo Zikuthandiza Kuti Anthu Azikhala Mwamtendere? 1/11
“Musaganize Kuti Ndamwalira,” 9/11
Buku la Jean Crespin Lonena za Anthu Ofera Chikhulupiriro, 3/11
Baibulo la King James, 12/11
SAYANSI
Moyo ndi Mphatso Yamtengo Wapatali, 5/11
Kodi Zinangochitika Zokha? 1/11, 2/11, 3/11, 4/11, 5/11, 6/11, 8/11, 9/11, 11/11
ZIMENE BAIBULO LIMANENA
Kodi Baibulo Limalimbikitsa Ukapolo? 7/11
Kodi Chikhulupiriro ndi Kuganiza Mwakuya Zimayenderana? 1/11
Kodi Mulungu Amasamalira Nyama? 12/11
Kodi Mulungu Ali Paliponse? 4/11
N’chifukwa Chiyani Mulungu Salola Akhristu Kumenya Nkhondo? 8/11
Zimene Mungachite Kuti Banja Lanu Liziyenda Bwino, 11/11
Kodi Sayansi ndi Baibulo Zimagwirizana? 2/11
Kudzizunza, 3/11
Kodi Tiziona Kuti Tsiku Lina Pamlungu Ndi Lopatulika? 9/11
Kodi Mumafuna Kuti Mwana Wanu Adzakhale Wotani Akadzakula? 10/11
N’chifukwa Chiyani Akhristu Oona Amadedwa? 5/11
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusamala ndi Zimene Timalankhula? 6/11
ZOCHITIKA PA DZIKO
Zokambirana Zokhudza Kusokonekera kwa Nyengo, 11/11
Zauchigawenga, 6/11
ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA
Kodi Ndimagwiritsira Ntchito Foni, Tv, Kompyuta Kapena Intaneti Mopitirira Malire? 1/11
Kodi Ndine Wolephera? 5/11
Kodi Ndingatani Kuti Anthu Azindikonda Ndikangokumana Nawo Koyamba? 6/11
Malo Ochezera a pa Intaneti, 7/11, 8/11
Kodi Chimafunika N’chiyani Kuti Phwando Likhale Losangalatsa? 12/11
Kodi Ndiyenera Kudziwa Chiyani Zokhudza Kusuta Fodya? 3/11
Kodi Ndi Anthu Ati Amene Ndingamacheze Nawo Momasuka? 4/11
Kodi Ndingasankhe Bwanji Mafilimu, Mabuku Komanso Nyimbo Zabwino? 11/11
Kodi Ndimadziwa Mfundo Zimene Ndimayendera? 10/11
Kodi Ndingadziwe Bwanji Anzanga Enieni? 9/11
N’chifukwa Chiyani Makolo Anga Sandilola Kupita Kokasangalala? 2/11