Zisonyezero za Voliyumu 81 ya Galamukani!
Zisonyezero za Voliyumu 81 ya Galamukani!
ACHINYAMATA AKUFUNSA
Angathaŵedi Ana Awo, 6/8, 12/8
Kodi Ndikhale ndi Khadi la Ngongole? 1/8
Kodi Ndisamukire Kudziko lina? 7/8
Kubereka Ana, 5/8
Kuboola Thupi, 4/8
Kuvutika Maganizo, 11/8
Kuvutitsidwa ndi Amuna Kapena Akazi, 9/8
N’chifukwa Chiyani Bwenzi Langa Linandikhumudwitsa? 3/8
N’chifukwa Chiyani Ndili Wochepa Thupi? 10/8
CHIPEMBEDZO
‘Iwo Anali Osangalatsa,’ 1/8
Kukhulupirira Mizimu—N’kothandiza Kapena N’kovulaza? 8/8
Pali zinthu zambiri zimene maso paokha sangaone, 9/8
CHUMA NDI NTCHITO
Kodi “Ntchito Yokhazikika” Idamka Kuti? 10/8
LINGALIRO LA BAIBULO
Chikhulupiriro Choona N’chiyani? 3/8
Kodi Kulambira Yesu N’koyenera? 4/8
Kodi Mulungu Amasandulika? 6/
Kodi Sayansi Ingabweretse Moyo Wosatha? 12/8
Kudzikongoletsa, 8/8
Kunama—Kodi Nthaŵi Zina N’kolungama? 2/8
Kusinkhasinkha Kumene Kumapindulitsa, 9/8
“Maseŵera Angozi,” 10/8
Njira Yogonjetsera Kutaya Mtima, 5/8
Nyenyezi Zolosera, 11/8
MAUNANSI A ANTHU
Kodi Chisoni Chiyenera Kusonyezedwa? 8/8
Mabanja Opanda Bambo, 2/8
Mmene Banja Lathu Linagwirizanirananso, 6/8
Mwetulirani—N’zothandiza kwa Inu! 7/8
Kuona Miyambo Yotchuka M’njira Yoyenera, 1/8
MAYIKO NDI ANTHU
AIDS mu Afirika, 5/8
Amayi Odwala AIDS Akusowa Pogwira, 1/8
Chivomezi! (Taiwan), 9/8
Thandizo kwa Ozunzidwa [Denmark], 1/8
MBONI ZA YEHOVA
Anawapulumutsa Lokumbakumba (Benin), 11/8
Anthu a ku Russia Akuyamikira Ufulu wa Kulambira, 3/8
Chikhulupiriro Cholimba M’kati mwa Mavuto (P. Esch), 4/8
Kuthandiza Achinyamata Kusiya Kupulupudza (France), 9/8
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Chimene Ndimaikirapo Mtima Kwambiri Ndicho Kukhalabe Wokhulupirika (A. Davidjuk), 10/8
Khama Langa Lofuna Kusankha Zinthu Mwanzeru (G. Sisson), 9/8
Kukhalabe Okhulupirika mu Ulamuliro Wankhanza (M. Dasevich), 10/8
Kuthana ndi Ziyeso Mwamphamvu ya Mulungu (S. Kozhemba), 12/8
Kuyesedwa kwa Chikhulupiriro ku Poland (J. Ferenc), 11/8
Loida Ayamba Kulankhula, 5/8
Ngakhale Ndili Wolumala Ndine Wosangala (K. Morozov), 12/8
SAYANSI
Kupanga Mapu Osonyeza Miyamba, 2/8
Thambo Lathu—Kodi Linangokhalako Mwamwayi? 10/8
Zimene Diso Palokha Silingaone, 9/8
UMOYO NDI MANKHWALA
AIDS mu Afirika, 5/8
Amayi Odwala AIDS Akusowa Pogwira, 1/8
Anamwino, 11/8
Chithandizo ndi Opaleshoni Zopanda Magazi, 1/8
Kodi Ndizimwa Asipilini Tsiku N’tsiku? 7/8
N’kusiyiranji Kusuta, 4/8
Kuthana ndi Matenda a Kachiwalo Kotchedwa Prostate, 12/8
Matenda Aakulu, 6/8
Mliri wa Matenda a Makoswe, 2/8
Mukadwala Chifukwa cha Mankhwala, 8/8
Njira Zochiritsira, 11/8
“Ufa!” (nkhani ya magazi), 5/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Kamzimbi (Mbalame), 2/8
Kodi Mbalame Ingam’phunzitsenji Mkaidi? 5/8
Mtundu Wodabwitsa wa Mbalame, 8/8
Nyamalikiti, 10/8
Nzimbe, 8/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Anthu Ovutika ndi Nkhondo Asintha, 2/8
Kodi kuona zithunzi zamaliseche pa intaneti kuli n’zoopsa zanji? Kodi zimenezi n’kuzipeŵa motani? 6/8
Kodi Makhalidwe ndi Otani Lerolino? 4/8
Kodi Moyo Ukutsikiratsikira Mtengo? 7/8
Kudzipha—Mliri Wobisika, 3/8
Kufuna Kuchotsa Boma la Vatican M’bungwe la UN, 11/8
Kusiyana Pakati pa Olemera ndi Osauka Kukukula, 2/8
Mabanja Opanda Bambo, 2/8
Mabomba Okwirira Pansi, 5/8
Malonda a Kuba Anthu, 1/8
Mavuto a Ana, 12/8
Nkhani Zokopa Zingaphetse Anthu, 7/8
Ukapolo Wamakono, 3/8
Zolinga za Olimpiki Zakanika? 9/8
ZOSIYANASIYANA
El Niño? 4/8
Kumeta Moyeretsa, 2/8
Nkhani za pa TV, 5/8
Zoopsa za Kukwera Matola, 7/8