Chikondi
Kodi anasonyeza bwanji chikondi?
Yer 31:3; Yoh 3:16; Aro 5:8; 1Yo 4:8, 19
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Ge 1:1, 26-31; 2:8, 9, 15, 16—Yehova anasonyeza chikondi pokonza dziko lapansili kukhala paradaiso ndipo anapatsa anthu oyambirira zinthu zambiri zabwino m’munda wa Edeni
-
Sl 104:27-30—Wamasalimo anayamikira Yehova chifukwa chosonyeza chikondi pa cholengedwa chilichonse
-
Kodi tingasonyeze bwanji chikondi?
Yoh 13:34, 35; 15:12, 13; 1Pe 4:8; 1Yo 4:10, 11; 5:3
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Mt 22:36-39—Yesu ananena za malamulo awiri aakulu kwambiri ndipo onsewo ndi okhudza chikondi
-
1Ak 13:1-8—Mtumwi Paulo anafotokoza kufunika kwa chikondi; komanso anatisonyeza zimene tingachite posonyeza chikondi
-